Chakwera, Chilima sakutayana pamene Chilima akukayimirira Chakwera ku South Korea
Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera watumiza wachiwiri wake, Dr. Saulos Klaus Chilima, kuti akamuyimirire msonkhano wa msonkhano womwe cholinga chake kulimbikitsa ubale and ntchito za malonda pakati pa mayiko a mu Africa ndi dziko la …